Русские видео

Сейчас в тренде

Иностранные видео


Скачать с ютуб Khalabe Odikira - The Morning Star (Official Video) в хорошем качестве

Khalabe Odikira - The Morning Star (Official Video) 8 месяцев назад


Если кнопки скачивания не загрузились НАЖМИТЕ ЗДЕСЬ или обновите страницу
Если возникают проблемы со скачиванием, пожалуйста напишите в поддержку по адресу внизу страницы.
Спасибо за использование сервиса savevideohd.ru



Khalabe Odikira - The Morning Star (Official Video)

Lyrics: 1. Zosautsa zochuluka okondedwa m'moyowu Kukumana ndi zipsinjo zosaneneka Kuyesetsa kupemphera ngati Mlungu saakumva Zafika povuta moyuwu kuwawa Kuyang’ana uko wachoka ndizogwetsa mphwayi Kuganiza zatsogolo mtima umasweka Nthawi zina ukaona ena zithu zikuwayendera Zimangopangitsa ‘we kukhumudwa Chorus Kaya nyengo ivute iwopse bwanji Ndi zinthu za kanthawi kanthawi kochepa Zisakuchotse ‘we pamaso pa Mulengi wako Khalabe odikira mkhulupire Akulonjeza kukhala nawe kukusamalira zinthu zikavuta Ngakhale lonjezano lake lichedwe bwanji Khalabe odikira mkhulupire 2. Zolilitsa tsiku ndi tsiku kuopsedwa m'moyowu Kunyozedwa ndiopembedza nao limodzi Komabe m'nyengo zotere kumbuka liripo bwenzi Bwenzi lopambana ndiye Yesu Akhala nawe poyenda akhala nawe pogona Akhala mawe mtendere ndinso polira Iye ali ndi chinsisi cha tsogolo la moyo wako Khalabe odikira mkhulupire ----------------------------------------------------- The Morning Star, Kawale, Lilongwe Audio by: Recall, Kuimba Mwamphamvu Studio Video by: Hope Channel Malawi ----------------------------------------------------- Share this video:    • Khalabe Odikira - The Morning Star (O...   Subscribe for more videos:    / @themorningstar-mw   Audio playlist:    • M'bandakucha - The Morning Star   ----------------------------------------------------- Connect with us: Facebook:   / themorningstarsingersmw   Instagram:   / themorningstar_mw   Whatsapp: https://whatsapp.com/channel/0029Va5V... Spotify - https://spotify.link/EC6GyW0v3xb E-mail: [email protected]

Comments