Русские видео

Сейчас в тренде

Иностранные видео


Скачать с ютуб CRUISE 5 ELIYA NZERU WILLIAM в хорошем качестве

CRUISE 5 ELIYA NZERU WILLIAM 3 года назад


Если кнопки скачивания не загрузились НАЖМИТЕ ЗДЕСЬ или обновите страницу
Если возникают проблемы со скачиванием, пожалуйста напишите в поддержку по адресу внизу страницы.
Спасибо за использование сервиса savevideohd.ru



CRUISE 5 ELIYA NZERU WILLIAM

Anthu ena amakhulupilira kuti ufiti kulibe - anthu amenewa sanakumane ndi a Eliya William. Iwe amatsimikiza kuti adatambako komanso adapangako using'anga. A Eliya anali mkulu wa bungwe la asing'anga ku Malawi kuyambila 1986 mpaka 1996. Iwo siabisa kuti achita zinthu zoopsya komanso aona zambiri kudzela mmatsenga. Iwo akutsindika kuti zambiri zimene timamva zokhudza amfiti ndizoona; amfiti amauluka kugwilitsa ntchito lichelo kapena tsache, ndondocha ndi anthu akufa amene amawathila mankhwala kuti achepe akatelo amawagwilitsa ntchito mmatsenga kuti azikaba ndalama kapena kulima kumunda, anthu amalodzana munjira zosiyanasiyana kuti wina afe kapena azikumana ndi matsoka. Nkhani yabwino ndiyakuti a Eliya zaufiti komanso using'anga adasiya ndipo pano adayamba kupemphela ku mpingo wa Zioni komwe adakwela mpaka kufika pa udindo wa Bishop.

Comments